Pokumbukira mtandawo lyrics
Pokumbukira mtandawo lyrics
Pokumbukira mtandawo
Ambuye ‘nandiferapo,
Ndiyesa zingochepazo
Ndinazitama kaleko.
Refrain: Amen, Aleluya repeated
Mndiletse, ndisatame ‘yi
Zachabe, koma imfayi;
Zijazo ndinakondazo
Ndazilekera mwaziwo.
Onani m’mutu, m’manjanso
Mudzera nsoni m’mwazimo.
A! panalibe kalelo
Wondibvalira mingayo.
Chinkana dziko lonselo
Lichepa ndithu mtulowo,
Chikondicho chagwirabe
Mtimanga, moyo, ndense ‘ne.
- Artist:Malawi Folk
See more