Angozo

Songs   2024-07-02 21:06:11

Angozo

(CHORUS)

Angozo

Safuna zoyambana Angozo

Angozo

Safuna zokangana Angozo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ndi ntondo ntondo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ntondo

(PIKSY)

Wodya zake alibe mulandu

Ali ndi tsoka wopanga za anthu

Zawo zikuyenda

Nsanje ndi matenda

Zawo amanena ndi anthu Angozo ndi ofewa

Angozo sadzatheka

Humble, selfless

Sathoka za udolo wawo,

Ndi katundu, Amfumu

Koma mmudzimu akulemera ndani?

(Ndi Angozo)

Akazi abwino amagomera ndani?

(Angozo)

Pakati pawo alibe stress ndani?

(Ndi Angozo)

Ndekuti awa angochedwa kupanga ziphokoso

I am the definition of Angozo

Chikhala nyerere you know bwenzi ndiri mdzodzo

Tsono dzimakomo kutseguka

Chikho chawo kusefuka

Zowapinga kupatuka

Ineyo ndi Angozo

(CHORUS)

Angozo

Safuna zoyambana Angozo

Angozo

Safuna zokangana Angozo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ndi ntondo ntondo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ntondo

(TAY GRIN)

Angozo mdi bad man

Wa pa easy koma otchuka ngati Gangnam

Ndi ma chick amahita ngati Van Dame

Sadzipopa ngati bubble gum

Mfana ozitsata (ingofunsafunsa akuuza)

Mfana ozisanja (Ona Motor akuphusha)

Mfana wa chikoka (Anthu onse mmudzi amamdziwa)

Angozo!

Olo mafana amatchula dzina

Amakwana, amathina

Anthu amadziwa ndi makina

Mitu yawo imayima

Angozo ndi Head-cleaner

Dziko limavina

Apapa china nchina

Ngakhale amene sakufuna apange salute

Angozo!

(CHORUS)

Angozo

Safuna zoyambana Angozo

Angozo

Safuna zokangana Angozo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ndi ntondo ntondo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ntondo

(LULU)

Angozo mmudzi nkhani ndi yawo

Kulima minda opanda mvula kukolola

Angozo mudzi ukamba za iwo

Mulungu analemba Angozo ngokolola

Ngakhale tsiku la ma dyelero

Azimayi amangofuna Angozo ayimbe ng'oma

Ena akuti ng'omanso ayi

Angozo tiwafuna pafupi ativinitse

Kuntero Ngozo ng'oma kuti Booo

(Ngozo ayimbe ng'oma oh oh)

Kuntero ngozo stepe kuti seee

(Ngozo ayimbe ng'oma oh oh)

Kuntero Ngozo ng'oma kuti Booo

(Ngozo ayimbe ng'oma oh oh)

Kuntero ngozo stepe kuti seee

(Ngozo ayimbe ng'oma oh oh)

Angozo amuna anzawo nsanje

Angozo modzichepetsa kuseka

Angozo sangamalize chitelera

Kuopa kuwadikira pa njira

(CHORUS)

Angozo

Safuna zoyambana Angozo

Angozo

Safuna zokangana Angozo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ndi ntondo ntondo

Angozo Angozo Angozo

Ndi ntondo ntondo

See more
Tay Grin more
  • country:Malawi
  • Languages:English, Chewa
  • Genre:
  • Official site:https://www.youtube.com/channel/UCHUjW4Wb8At8RD3jaGX3unA
  • Wiki:https://www.malawi-music.com/T/3-tay-grin
Tay Grin Lyrics more
Excellent Songs recommendation
Popular Songs
Copyright 2023-2024 - www.lyricf.com All Rights Reserved